1 Petulo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo m’busa wamkulu+ akadzaonekera, mudzalandira mphoto* yosafwifwa,+ yaulemerero.+