Salimo 92:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 92 Ndi bwino kuyamika inu Yehova,+Ndi kuimba nyimbo zotamanda dzina lanu, inu Wam’mwambamwamba.+