Genesis 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Mulungu anati: “N’chiyani chimene wachitachi? Tamvera tsono. Magazi a m’bale wako akundilirira munthaka.+ Deuteronomo 32:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”
10 Pamenepo Mulungu anati: “N’chiyani chimene wachitachi? Tamvera tsono. Magazi a m’bale wako akundilirira munthaka.+
43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”