Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 65:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+

      Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+

  • Yesaya 17:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mitundu ya anthu+ idzasokosera ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula,+ ndipo iwo adzathawira kutali. Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo m’mapiri ndiponso adzauluzika ngati tizitsotso touluzika ndi mphepo yamkuntho.+

  • Yesaya 57:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Koma anthu oipa ali ngati nyanja imene ikuwinduka, imene ikukanika kukhala bata, imene madzi ake akuvundula zomera za m’nyanjamo ndiponso matope.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena