Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe,+

      Ndiponso n’chifukwa chiyani mitundu ya anthu ikung’ung’udza za chinthu chopanda pake?+

  • Yesaya 17:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsoka kwa mitundu ya anthu ambirimbiri amene akuchita chipwirikiti, amene akuwinduka ngati nyanja. Tsoka kwa magulu a mitundu ya anthu aphokoso, amene akusokosera ngati mkokomo wa madzi amphamvu.+

  • Yesaya 57:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Koma anthu oipa ali ngati nyanja imene ikuwinduka, imene ikukanika kukhala bata, imene madzi ake akuvundula zomera za m’nyanjamo ndiponso matope.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena