Chivumbulutso 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako mngelo wachisanu analiza lipenga+ lake. Ndipo ndinaona nyenyezi+ imene inagwera kudziko lapansi kuchokera kumwamba. Nyenyeziyo inapatsidwa kiyi+ wa dzenje+ lolowera kuphompho. Chivumbulutso 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo ndinaona mngelo akutsika kuchokera kumwamba ali ndi kiyi wa paphompho+ ndi unyolo waukulu m’dzanja lake.
9 Kenako mngelo wachisanu analiza lipenga+ lake. Ndipo ndinaona nyenyezi+ imene inagwera kudziko lapansi kuchokera kumwamba. Nyenyeziyo inapatsidwa kiyi+ wa dzenje+ lolowera kuphompho.
20 Ndipo ndinaona mngelo akutsika kuchokera kumwamba ali ndi kiyi wa paphompho+ ndi unyolo waukulu m’dzanja lake.