Luka 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ziwandazo zinali kumuchonderera+ kuti asazilamule kuti zipite kuphompho.+ Chivumbulutso 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dzombelo lili ndi mfumu. Mfumuyo ndiye mngelo wa phompho.+ M’Chiheberi, dzina lake ndi Abadoni, koma m’Chigiriki ali ndi dzina lakuti Apoliyoni.+
11 Dzombelo lili ndi mfumu. Mfumuyo ndiye mngelo wa phompho.+ M’Chiheberi, dzina lake ndi Abadoni, koma m’Chigiriki ali ndi dzina lakuti Apoliyoni.+