Zekariya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’mbali mwa choikapo nyalecho muli mitengo iwiri ya maolivi.+ Umodzi uli mbali ya kudzanja lamanja la mbale yolowayo, ndipo wina uli kumanzere kwa mbaleyo.” Zekariya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndinafunsa mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja kuti: “Kodi mitengo iwiri ya maolivi, imene wina uli kudzanja lamanja ndi wina kumanzere kwa choikapo nyalechi, ikuimira chiyani?”+
3 M’mbali mwa choikapo nyalecho muli mitengo iwiri ya maolivi.+ Umodzi uli mbali ya kudzanja lamanja la mbale yolowayo, ndipo wina uli kumanzere kwa mbaleyo.”
11 Ndiyeno ndinafunsa mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja kuti: “Kodi mitengo iwiri ya maolivi, imene wina uli kudzanja lamanja ndi wina kumanzere kwa choikapo nyalechi, ikuimira chiyani?”+