Zekariya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’mbali mwa choikapo nyalecho muli mitengo iwiri ya maolivi.+ Umodzi uli mbali ya kudzanja lamanja la mbale yolowayo, ndipo wina uli kumanzere kwa mbaleyo.” Chivumbulutso 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mboni zimenezi zikuimiridwa ndi mitengo iwiri ya maolivi,+ ndi zoikapo nyale ziwiri,+ ndipo mbonizo zaimirira pamaso pa Ambuye wa dziko lapansi.+
3 M’mbali mwa choikapo nyalecho muli mitengo iwiri ya maolivi.+ Umodzi uli mbali ya kudzanja lamanja la mbale yolowayo, ndipo wina uli kumanzere kwa mbaleyo.”
4 Mboni zimenezi zikuimiridwa ndi mitengo iwiri ya maolivi,+ ndi zoikapo nyale ziwiri,+ ndipo mbonizo zaimirira pamaso pa Ambuye wa dziko lapansi.+