Chivumbulutso 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu+ zambiri. Anali ndi dzina+ lolembedwa limene wina aliyense sanali kulidziwa, koma iye yekha.
12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu+ zambiri. Anali ndi dzina+ lolembedwa limene wina aliyense sanali kulidziwa, koma iye yekha.