Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma dziko lapansi linali litaipa pamaso pa Mulungu woona,+ ndipo linadzaza ndi chiwawa.+

  • Salimo 53:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:

      “Kulibe Yehova.”+

      Anthu oterewa amachita zoipa, ndipo amachita zinthu zonyansa zogwirizana ndi kupanda chilungamo kwawo.+

      Palibe amene akuchita zabwino.+

  • Yeremiya 6:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Onse ndi anthu ouma khosi kwambiri,+ oyenda uku ndi uku ngati anthu amiseche.+ Iwo ali ngati mkuwa ndi chitsulo. Onsewo ndi anthu owononga.+

  • Yeremiya 51:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Ine ndikuthira nkhondo iwe+ phiri lowononga,+ amene wawononga dziko lonse lapansi.+ Ndidzatambasula dzanja langa ndi kukuthira nkhondo. Ndidzakugubuduza kukuchotsa pamatanthwe ndipo ndidzakusandutsa phiri lotenthedwa ndi moto,” watero Yehova.+

  • Zefaniya 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno ndinati, ‘Mosakayikira udzandiopa ndipo udzalola kulangizidwa’+ kuti malo ake okhala asawonongedwe,+ pakuti ndidzamuimba mlandu wa zonsezi.+ Koma zinthu zawo zonse zimene anali kuchita zinali zowawonongetsa ndipo anazichitadi mofulumira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena