Yesaya 49:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachititsa m’kamwa mwanga kukhala ngati lupanga lakuthwa.+ Anandibisa mumthunzi+ wa dzanja lake.+ Anandisandutsa muvi wonola bwino. Anandibisa m’kachikwama kake koikamo mivi.
2 Iye anachititsa m’kamwa mwanga kukhala ngati lupanga lakuthwa.+ Anandibisa mumthunzi+ wa dzanja lake.+ Anandisandutsa muvi wonola bwino. Anandibisa m’kachikwama kake koikamo mivi.