Chivumbulutso 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa chifukwa chimenechi, kondwerani kumwamba inu ndi inu okhala kumeneko!+ Tsoka+ dziko lapansi ndi nyanja,+ chifukwa Mdyerekezi watsikira kwa inu, ndipo ali ndi mkwiyo waukulu podziwa kuti wangotsala ndi kanthawi kochepa.”+
12 Pa chifukwa chimenechi, kondwerani kumwamba inu ndi inu okhala kumeneko!+ Tsoka+ dziko lapansi ndi nyanja,+ chifukwa Mdyerekezi watsikira kwa inu, ndipo ali ndi mkwiyo waukulu podziwa kuti wangotsala ndi kanthawi kochepa.”+