Luka 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Simoni, Simoni! Ndithu Satana+ akufuna anthu inu, kuti akupeteni ngati tirigu.+ Chivumbulutso 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo chinjokacho chinakwiya ndi mkazi uja,+ moti chinapita kukachita nkhondo ndi otsala a mbewu yake, amene amasunga malamulo a Mulungu, amenenso ali ndi ntchito yochitira umboni+ za Yesu.
17 Ndipo chinjokacho chinakwiya ndi mkazi uja,+ moti chinapita kukachita nkhondo ndi otsala a mbewu yake, amene amasunga malamulo a Mulungu, amenenso ali ndi ntchito yochitira umboni+ za Yesu.