Yesaya 66:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mumzinda mukumveka phokoso lachisokonezo, phokoso lochokera kukachisi.+ Limeneli ndi phokoso losonyeza kuti Yehova akubwezera adani ake chilango chowayenerera.+ Chivumbulutso 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno mngelo wa 7 anakhuthulira mbale yake pampweya.+ Atatero, kunamveka mawu ofuula+ kuchokera m’malo opatulika, kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Zachitika!”
6 Mumzinda mukumveka phokoso lachisokonezo, phokoso lochokera kukachisi.+ Limeneli ndi phokoso losonyeza kuti Yehova akubwezera adani ake chilango chowayenerera.+
17 Ndiyeno mngelo wa 7 anakhuthulira mbale yake pampweya.+ Atatero, kunamveka mawu ofuula+ kuchokera m’malo opatulika, kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Zachitika!”