Yeremiya 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova Mulungu wa Isiraeli anandiuza kuti: “Landira chikho ichi chimene chili m’dzanja langa. Mmenemu muli vinyo wa mkwiyo ndipo ukamwetse mitundu yonse imene ndikukutumizako.+ Chivumbulutso 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiye chimodzi cha zamoyo zinayi+ zija chinapatsa angelo 7 amenewo mbale zagolide 7, zodzaza ndi mkwiyo wa Mulungu,+ amene adzakhala ndi moyo kwamuyaya.+
15 Yehova Mulungu wa Isiraeli anandiuza kuti: “Landira chikho ichi chimene chili m’dzanja langa. Mmenemu muli vinyo wa mkwiyo ndipo ukamwetse mitundu yonse imene ndikukutumizako.+
7 Ndiye chimodzi cha zamoyo zinayi+ zija chinapatsa angelo 7 amenewo mbale zagolide 7, zodzaza ndi mkwiyo wa Mulungu,+ amene adzakhala ndi moyo kwamuyaya.+