Danieli 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Ku mapeto kwa ufumu wawo, uchimo wawo ukadzafika pachimake, padzauka mfumu ya maonekedwe oopsa ndiponso yomvetsa zinthu zovuta kumva.+
23 “Ku mapeto kwa ufumu wawo, uchimo wawo ukadzafika pachimake, padzauka mfumu ya maonekedwe oopsa ndiponso yomvetsa zinthu zovuta kumva.+