Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pamene ndinali kuyang’anitsitsa nyangazo, ndinaona kuti nyanga ina yaing’ono yamera+ pakati pa nyangazo. Nyanga zitatu pa nyangazi zinazulidwa pamalo amene nyanga yaing’onoyo inamera. Nyangayi inali ndi maso ngati a munthu, ndipo inali ndi pakamwa polankhula mawu odzitukumula.+

  • Danieli 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Pa nthawi imeneyo, ndinapitirizabe kuyang’ana chifukwa ndinali kumva mawu odzitukumula amene nyanga ija inali kulankhula.+ Ndinapitirizanso kuyang’ana kufikira pamene chilombocho chinaphedwa ndipo thupi lake linaponyedwa pamoto n’kuwonongedwa.+

  • Chivumbulutso 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako ndinaona chilombo+ china chikutuluka pansi pa dziko lapansi.+ Chinali ndi nyanga ziwiri ngati mwana wa nkhosa, koma chinayamba kulankhula ngati chinjoka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena