48 “Kumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo zidzafuula mosangalala chifukwa cha kugwa kwa Babulo,+ pakuti ofunkha zinthu zake adzafika kuchokera kumpoto,”+ watero Yehova.
12 Pa chifukwa chimenechi, kondwerani kumwamba inu ndi inu okhala kumeneko!+ Tsoka+ dziko lapansi ndi nyanja,+ chifukwa Mdyerekezi watsikira kwa inu, ndipo ali ndi mkwiyo waukulu podziwa kuti wangotsala ndi kanthawi kochepa.”+