Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake. Yeremiya 51:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 “Babulo sanangophetsa anthu a mu Isiraeli okha+ koma anaphetsanso anthu a padziko lonse lapansi m’Babulomo.+
6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.
49 “Babulo sanangophetsa anthu a mu Isiraeli okha+ koma anaphetsanso anthu a padziko lonse lapansi m’Babulomo.+