Chivumbulutso 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine Yohane, ndine amene ndinali kumva ndi kuona zinthu zimenezi. Ndipo nditamva ndi kuona, ndinagwada n’kuwerama kuti ndilambire+ pamapazi a mngelo amene anali kundionetsa zinthu zimenezi.
8 Ine Yohane, ndine amene ndinali kumva ndi kuona zinthu zimenezi. Ndipo nditamva ndi kuona, ndinagwada n’kuwerama kuti ndilambire+ pamapazi a mngelo amene anali kundionetsa zinthu zimenezi.