Machitidwe 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Petulo anamuimiritsa, ndi kunena kuti: “Imirira, inenso ndine munthu chabe.”+ Chivumbulutso 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iye anandiuza kuti: “Samala! Usatero ayi! Inetu ndangokhala kapolo mnzako, ndi wa abale ako amene ndiwo aneneri,+ ndi wa anthu amene akusunga mawu a mumpukutu umenewu. Lambira Mulungu.”+
9 Koma iye anandiuza kuti: “Samala! Usatero ayi! Inetu ndangokhala kapolo mnzako, ndi wa abale ako amene ndiwo aneneri,+ ndi wa anthu amene akusunga mawu a mumpukutu umenewu. Lambira Mulungu.”+