2 Atesalonika 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo, wosamvera malamuloyo adzaonekera ndithu, amene Ambuye Yesu adzamuthetsa ndi mzimu wa m’kamwa mwake,+ pomuwonongeratu pa nthawi imene kukhalapo kwa Yesuyo kudzaonekere.+ Chivumbulutso 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’dzanja lake lamanja anali ndi nyenyezi 7.+ M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse.+ Nkhope yake inali yowala ngati dzuwa limene likuwala kwambiri.+
8 Pamenepo, wosamvera malamuloyo adzaonekera ndithu, amene Ambuye Yesu adzamuthetsa ndi mzimu wa m’kamwa mwake,+ pomuwonongeratu pa nthawi imene kukhalapo kwa Yesuyo kudzaonekere.+
16 M’dzanja lake lamanja anali ndi nyenyezi 7.+ M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse.+ Nkhope yake inali yowala ngati dzuwa limene likuwala kwambiri.+