52 m’kamphindi, m’kuphethira kwa diso, pa kulira kwa lipenga lomaliza. Pakuti lipengalo+ lidzalira, ndipo akufa adzaukitsidwa osakhoza kuwonongeka, ndipo tidzasandulika.
16 Chifukwa Ambuye mwini adzatsika kumwamba,+ ndi mfuu yolamula ya mawu a mkulu wa angelo,+ ndi lipenga+ la Mulungu. Ndipo amene anafa mwa Khristu adzauka choyamba.+