Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 12
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

1 Akorinto 12:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:1, 37

1 Akorinto 12:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 2:12
  • +1Ak 8:4; Aga 4:8; 1At 1:9; 1Pe 4:3
  • +Sl 115:5; Hab 2:18

1 Akorinto 12:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mko 9:39; 1Yo 4:3
  • +Mt 16:17; 1Yo 4:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2007, tsa. 21

1 Akorinto 12:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 2:4; 1Pe 4:10
  • +Aef 4:4

1 Akorinto 12:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:7; Aef 4:11
  • +Aef 4:5

1 Akorinto 12:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 2:43
  • +1Pe 4:11
  • +Aef 4:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2011, ptsa. 24-25

1 Akorinto 12:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:26; Aef 4:7

1 Akorinto 12:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 1:17
  • +1Ak 14:6; 2Ak 8:7

1 Akorinto 12:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 13:2; 2Ak 4:13
  • +Mac 3:7; 28:9

1 Akorinto 12:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 2:4
  • +Aro 12:6
  • +1Ak 14:29
  • +1Yo 4:1
  • +Mac 10:46; 1Ak 14:18
  • +1Ak 14:26

1 Akorinto 12:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:6
  • +Aro 12:3; 1Ak 7:7; Aef 4:7
  • +Ahe 2:4

1 Akorinto 12:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:5
  • +Aro 7:4; 1Ak 10:16; Aef 4:12

1 Akorinto 12:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 4:5
  • +Yoh 4:14; 7:37; Chv 22:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 110

1 Akorinto 12:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 4:16

1 Akorinto 12:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 4:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    8/2020, ptsa. 23-24

1 Akorinto 12:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 5:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    8/2020, ptsa. 23-24

1 Akorinto 12:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 20:12; 1Ak 15:38

1 Akorinto 12:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:4; 1Ak 12:14

1 Akorinto 12:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:14

1 Akorinto 12:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/1996, tsa. 20

1 Akorinto 12:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mla 9:15; Aro 9:23; 1Ak 1:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2014, tsa. 24

    10/15/1997, ptsa. 14-15

1 Akorinto 12:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 3:7, 21; 2Ti 2:20

1 Akorinto 12:24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/1999, tsa. 20

1 Akorinto 12:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:10; Aef 4:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 19

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2007, tsa. 20

    5/15/2004, tsa. 19

    10/15/1986, tsa. 23

1 Akorinto 12:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 6:2; Ahe 13:3; 1Pe 5:9
  • +Aro 8:17
  • +Aro 12:15; 1Pe 3:8; 4:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 19

1 Akorinto 12:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:5; Aef 1:23; Akl 1:24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1995, tsa. 11

1 Akorinto 12:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 12:18
  • +Aef 2:20
  • +Mac 13:1
  • +Aef 4:11
  • +Aga 3:5
  • +Mac 5:16
  • +Mac 18:27
  • +Aro 12:8; 1Ak 3:10; Ahe 13:17
  • +Mac 2:6

1 Akorinto 12:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:4
  • +1Ak 14:5

1 Akorinto 12:31

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:1
  • +1Ak 13:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2009, ptsa. 26-27

    2/15/1999, ptsa. 22-23

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

1 Akor. 12:11Ak 14:1, 37
1 Akor. 12:2Aef 2:12
1 Akor. 12:21Ak 8:4; Aga 4:8; 1At 1:9; 1Pe 4:3
1 Akor. 12:2Sl 115:5; Hab 2:18
1 Akor. 12:3Mko 9:39; 1Yo 4:3
1 Akor. 12:3Mt 16:17; 1Yo 4:2
1 Akor. 12:4Ahe 2:4; 1Pe 4:10
1 Akor. 12:4Aef 4:4
1 Akor. 12:5Aro 12:7; Aef 4:11
1 Akor. 12:5Aef 4:5
1 Akor. 12:6Mac 2:43
1 Akor. 12:61Pe 4:11
1 Akor. 12:6Aef 4:6
1 Akor. 12:71Ak 14:26; Aef 4:7
1 Akor. 12:8Aef 1:17
1 Akor. 12:81Ak 14:6; 2Ak 8:7
1 Akor. 12:91Ak 13:2; 2Ak 4:13
1 Akor. 12:9Mac 3:7; 28:9
1 Akor. 12:10Ahe 2:4
1 Akor. 12:10Aro 12:6
1 Akor. 12:101Ak 14:29
1 Akor. 12:101Yo 4:1
1 Akor. 12:10Mac 10:46; 1Ak 14:18
1 Akor. 12:101Ak 14:26
1 Akor. 12:111Ak 12:6
1 Akor. 12:11Aro 12:3; 1Ak 7:7; Aef 4:7
1 Akor. 12:11Ahe 2:4
1 Akor. 12:12Aro 12:5
1 Akor. 12:12Aro 7:4; 1Ak 10:16; Aef 4:12
1 Akor. 12:13Aef 4:5
1 Akor. 12:13Yoh 4:14; 7:37; Chv 22:17
1 Akor. 12:14Aef 4:16
1 Akor. 12:15Aef 4:25
1 Akor. 12:16Aef 5:30
1 Akor. 12:18Miy 20:12; 1Ak 15:38
1 Akor. 12:19Aro 12:4; 1Ak 12:14
1 Akor. 12:201Ak 12:14
1 Akor. 12:22Mla 9:15; Aro 9:23; 1Ak 1:26
1 Akor. 12:23Ge 3:7, 21; 2Ti 2:20
1 Akor. 12:25Aro 12:10; Aef 4:25
1 Akor. 12:26Aga 6:2; Ahe 13:3; 1Pe 5:9
1 Akor. 12:26Aro 8:17
1 Akor. 12:26Aro 12:15; 1Pe 3:8; 4:13
1 Akor. 12:27Aro 12:5; Aef 1:23; Akl 1:24
1 Akor. 12:281Ak 12:18
1 Akor. 12:28Aef 2:20
1 Akor. 12:28Mac 13:1
1 Akor. 12:28Aef 4:11
1 Akor. 12:28Aga 3:5
1 Akor. 12:28Mac 5:16
1 Akor. 12:28Mac 18:27
1 Akor. 12:28Aro 12:8; 1Ak 3:10; Ahe 13:17
1 Akor. 12:28Mac 2:6
1 Akor. 12:301Ak 14:4
1 Akor. 12:301Ak 14:5
1 Akor. 12:311Ak 14:1
1 Akor. 12:311Ak 13:8
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
1 Akorinto 12:1-31

1 Akorinto

12 Tsopano abale, ponena za mphatso zauzimu,+ sindikufuna kuti mukhale osadziwa. 2 Mukudziwa kuti pamene munali a mitundu ina,+ munali kutsogoleredwa m’njira zosiyanasiyana ku mafano+ osalankhula.+ 3 Choncho ndikufuna mudziwe kuti palibe wolankhula mwa mzimu wa Mulungu amene anganene kuti: “Yesu ndi wotembereredwa!”+ Palibenso amene anganene popanda mzimu woyera kuti: “Yesu ndiye Ambuye!”+

4 Tsopano mphatso zilipo zamitundumitundu,+ koma mzimu ndi umodzi,+ 5 ndipo pali mautumiki osiyanasiyana,+ koma Ambuye ndi mmodzi.+ 6 Palinso ntchito zosiyanasiyana,+ koma Mulungu amene amachita ntchito zonsezo mwa anthu onse+ ndi mmodzi.+ 7 Tsopano ntchito za mzimu zimapatsidwa kwa munthu aliyense pa cholinga chopindulitsa.+ 8 Mwachitsanzo, mwa mzimu wina amapatsidwa mawu anzeru,+ ndipo wina amapatsidwa mawu ozindikira+ mwa mzimu womwewo. 9 Mwa mzimu womwewonso wina amapatsidwa chikhulupiriro,+ wina mphatso za kuchiritsa.+ 10 Winanso amapatsidwa mphatso yochita ntchito zamphamvu,+ wina kunenera,+ wina kuzindikira+ mawu ouziridwa,+ wina kulankhula malilime osiyanasiyana,+ ndiponso wina kumasulira+ malilime. 11 Koma ntchito zonsezi, mzimu umodzimodziwo+ ndiwo umazichita, pogawira+ aliyense payekha malinga ndi chifuniro cha mzimuwo.+

12 Pakuti mofanana ndi thupi lomwe ndi limodzi koma lili ndi ziwalo zambiri, ndipo ziwalo zonse za thupi, ngakhale ndi zambiri, zimapanga thupi limodzi,+ ndi mmenenso Khristu alili.+ 13 Pakuti ndi mzimu umodzi, tonsefe tinabatizidwa+ kukhala thupi limodzi, kaya tikhale Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena mfulu, ndipo tonsefe tinamwetsedwa+ mzimu umodzi.

14 Ndithudi, thupi si chiwalo chimodzi, koma zambiri.+ 15 Ngati phazi linganene kuti: “Popeza sindine dzanja, sindili mbali ya thupi,” chimenecho si chifukwa chopangitsa phazi kusakhala mbali ya thupi.+ 16 Ndipo ngati khutu linganene kuti: “Popeza sindine diso, sindili mbali ya thupi,” chimenecho si chifukwa chopangitsa khutu kusakhala mbali ya thupi.+ 17 Thupi lonse likanakhala diso, kodi mphamvu ya kumva ikanakhala kuti? Thupi lonse likanakhala khutu, kodi bwenzi tikumanunkhiza ndi chiyani? 18 Koma Mulungu anaika ziwalo m’thupi, chilichonse m’malo ake, mmene iye anafunira.+

19 Zonsezo zikanakhala chiwalo chimodzi,+ nanga thupi likanakhala kuti? 20 M’malomwake, ziwalozo n’zambiri,+ koma thupi ndi limodzi. 21 Diso silingauze dzanja kuti: “Ndilibe nawe ntchito,” kapenanso, mutu sungauze mapazi kuti: “Ndilibe nanu ntchito.” 22 Koma ziwalo za thupi zimene zimaoneka ngati zofooka+ ndizo zofunika. 23 Ndipo mbali za thupi zimene timaziona ngati zosalemekezeka kwambiri, n’zimene timazipatsa ulemu wochuluka,+ chotero mbali zathu zosaoneka bwino zimaoneka bwino kwambiri, 24 pamene mbali zathu zooneka bwino kale sizifunikira kalikonse. Ngakhale zili choncho, Mulungu analumikiza bwino thupi lonse, kuika ulemu wochuluka pa mbali imene inalibe ulemuwo, 25 kuti thupi lisakhale logawanika, koma ziwalo zake zisamalirane mofanana.+ 26 Ndipo chiwalo chimodzi chikavutika, ziwalo zina zonse zimavutikira nacho limodzi,+ komanso chiwalo chimodzi chikalemekezedwa,+ ziwalo zina zonse zimasangalalira nacho limodzi.+

27 Tsopano inu ndinu thupi la Khristu, ndipo aliyense wa inu ndi chiwalo cha thupilo.+ 28 Mulungu waika ziwalo zosiyanasiyana mumpingo.+ Choyamba atumwi,+ chachiwiri aneneri,+ chachitatu aphunzitsi,+ kenako ntchito zamphamvu,+ mphatso za kuchiritsa,+ utumiki wothandiza anthu,+ luso loyendetsa zinthu,+ ndi malilime osiyanasiyana.+ 29 Sikuti onse angakhale atumwi, angatero ngati? Sikuti onse angakhale aneneri, angatero ngati? Sikuti onse angakhale aphunzitsi, angatero ngati? Si onse amachita ntchito zamphamvu, ndi onse ngati? 30 Si onse amene ali ndi mphatso za kuchiritsa, ndi onse ngati? Si onse amalankhula malilime,+ ndi onse ngati? Sikuti onse ndi omasulira,+ ndi onse ngati? 31 M’malomwake, pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zazikulu.+ Komabe, ine ndikuonetsani njira yopambana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena