Masalimo
ג [Giʹmel]
ה [Heʼ]
ז [Zaʹyin]
4 Iye wakonza zoti ntchito zake zodabwitsa zizikumbukiridwa.+
ח [Chehth]
Yehova ndi wachisomo ndiponso wachifundo.+
ט [Tehth]
5 Wapereka chakudya kwa anthu omuopa.+
י [Yohdh]
Iye adzakumbukira pangano lake nthawi zonse.+
כ [Kaph]
6 Wafotokozera anthu ake mphamvu za ntchito zake,+
ל [Laʹmedh]
Mwa kuwapatsa cholowa cha mitundu ina ya anthu.+
מ [Mem]
7 Ntchito za manja ake zimadziwika ndi choonadi ndiponso chiweruzo.+
נ [Nun]
Malamulo onse amene amapereka ndi odalirika.+
ס [Saʹmekh]
8 Ndi ochirikizika bwino mpaka muyaya, ndithu mpaka kalekale,+
ע [ʽAʹyin]
Ndipo amawapereka m’choonadi ndiponso molungama.+
פ [Peʼ]
צ [Tsa·dhehʹ]
Wakhazikitsa pangano lake mpaka kalekale.+
ק [Qohph]
Dzina lake ndi loyera ndi lochititsa mantha.+
ר [Rehsh]
10 Chiyambi cha nzeru ndicho kuopa Yehova.+
ש [Sin]
Onse otsatira malamulo a Mulungu ndi ozindikira.+
ת [Taw]
Iye ayenera kutamandidwa mpaka muyaya.+