-
Machitidwe 7:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mitu ya mabanjayo inachitira nsanje Yosefe+ nʼkumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+ 10 ndipo anamupulumutsa mʼmavuto ake onse. Komanso ankamukonda ndipo ankamuthandiza kuti azichita zinthu mwanzeru pamaso pa Farao mfumu ya Iguputo. Faraoyo anapatsa Yosefe udindo woti aziyangʼanira Iguputo ndi nyumba yake yonse.+
-