Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Nayenso Semu anabereka ana ndipo anakhala kholo la ana onse a Ebere.+ Semu anali mngʼono wake wa Yafeti, amene anali wamkulu pa onse.*

  • Genesis 11:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iyi ndi mbiri ya Semu.+

      Semu anali ndi zaka 100 pamene anabereka Aripakisadi,+ patatha zaka ziwiri chigumula chitachitika.

  • Luka 3:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamene Yesu+ anayamba ntchito yake anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankadziwa kuti Yesu anali mwana

      wa Yosefe,+

      mwana wa Heli,

  • Luka 3:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 mwana wa Kainani,

      mwana wa Aripakisadi,+

      mwana wa Semu,+

      mwana wa Nowa,+

      mwana wa Lameki,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena