Mateyu 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yakobo anabereka Yosefe mwamuna wake wa Mariya, amene anabereka Yesu,+ wotchedwa Khristu.+ Mateyu 13:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Kodi uyu si mwana wa kalipentala uja?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo azichimwene ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?+ Luka 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zitatero onse anayamba kumutamanda komanso anadabwa ndi mawu ogwira mtima amene anatuluka pakamwa pake,+ moti ankanena kuti: “Kodi si mwana wa Yosefe ameneyu?”+ Yohane 6:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iwo anayamba kunena kuti: “Kodi uyu si Yesu mwana wa Yosefe, amene bambo ake ndi mayi ake tikuwadziwa?+ Nanga bwanji pano akunena kuti, ‘Ndinachokera kumwambaʼ?”
55 Kodi uyu si mwana wa kalipentala uja?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo azichimwene ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?+
22 Zitatero onse anayamba kumutamanda komanso anadabwa ndi mawu ogwira mtima amene anatuluka pakamwa pake,+ moti ankanena kuti: “Kodi si mwana wa Yosefe ameneyu?”+
42 Iwo anayamba kunena kuti: “Kodi uyu si Yesu mwana wa Yosefe, amene bambo ake ndi mayi ake tikuwadziwa?+ Nanga bwanji pano akunena kuti, ‘Ndinachokera kumwambaʼ?”