Genesis 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Patapita nthawi, Nowa anabereka ana aamuna atatu, Semu, Hamu ndi Yafeti.+ Genesis 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Hamu anali Kusi, Miziraimu,+ Puti+ ndi Kanani.+