5 Rubeni+ anali mwana woyamba kubadwa wa Isiraeli. Ana aamuna a Rubeni+ anali awa: Hanoki amene anali kholo la banja la Ahanoki, Palu amene anali kholo la banja la Apalu, 6 Hezironi amene anali kholo la banja la Ahezironi ndi Karami amene anali kholo la banja la Akarami.