12 Ana aamuna a Simiyoni+ potengera mabanja awo anali awa: Nemueli amene anali kholo la banja la Anemueli, Yamini amene anali kholo la banja la Ayamini, Yakini amene anali kholo la banja la Ayakini, 13 Zera amene anali kholo la banja la Azera ndi Shauli amene anali kholo la banja la Ashauli.