Numeri 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana aamuna a Simiyoni+ mwa mabanja awo anali awa: Nemueli+ amene anali kholo la banja la Anemueli, Yamini+ amene anali kholo la banja la Ayamini, Yakini+ amene anali kholo la banja la Ayakini,
12 Ana aamuna a Simiyoni+ mwa mabanja awo anali awa: Nemueli+ amene anali kholo la banja la Anemueli, Yamini+ amene anali kholo la banja la Ayamini, Yakini+ amene anali kholo la banja la Ayakini,