Numeri 26:23, 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana aamuna a Isakara+ potengera mabanja awo anali awa: Tola+ amene anali kholo la banja la Atola, Puva amene anali kholo la banja la Apuna, 24 Yasubi amene anali kholo la banja la Ayasubi ndi Simironi amene anali kholo la banja la Asimironi. 1 Mbiri 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Isakara analipo 4: Tola, Puwa, Yasubi ndi Simironi.+
23 Ana aamuna a Isakara+ potengera mabanja awo anali awa: Tola+ amene anali kholo la banja la Atola, Puva amene anali kholo la banja la Apuna, 24 Yasubi amene anali kholo la banja la Ayasubi ndi Simironi amene anali kholo la banja la Asimironi.