-
Numeri 26:44, 45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Ana aamuna a Aseri+ potengera mabanja awo anali awa: Imuna amene anali kholo la banja la Aimuna, Isivi amene anali kholo la banja la Aisivi ndi Beriya amene anali kholo la banja la Aberiya. 45 Ana aamuna a Beriya anali Hiberi amene anali kholo la banja la Ahiberi ndi Malikieli amene anali kholo la banja la Amalikieli.
-