Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 30:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Ndasangalala kwambiri! Akazi adzanena kuti ndine wosangalala.”+ Choncho Leya anapatsa mwanayo dzina lakuti Aseri.*+

  • Genesis 35:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ana amene Zilipa kapolo wa Leya anaberekera Yakobo anali Gadi ndi Aseri. Ana aamuna amene Yakobo anabereka ku Padani-aramu ndi amenewa.

  • Genesis 46:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ana a Aseri+ anali Imuna, Isiva, Isivi ndi Beriya ndipo mchemwali wawo anali Sera.

      Ana a Beriya anali Hiberi ndi Malikieli.+

  • 1 Mbiri 7:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ana a Aseri anali Imuna, Isiva, Isivi ndi Beriya+ ndipo mchemwali wawo anali Sera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena