Genesis 31:17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Yakobo anakweza ana ake ndi akazi ake pangamila.+ 18 Atatero anayamba kutenga ziweto zake zonse ndi katundu wake yense amene anapeza+ ku Padani-aramu, nʼkunyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani kwa Isaki bambo ake.+ Genesis 47:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Farao anafunsa abale ake a Yosefe aja kuti: “Kodi mumagwira ntchito yanji?” Iwo anayankha Farao kuti: “Akapolo anufe timaweta nkhosa ngati mmene ankachitira makolo athu.”+
17 Kenako Yakobo anakweza ana ake ndi akazi ake pangamila.+ 18 Atatero anayamba kutenga ziweto zake zonse ndi katundu wake yense amene anapeza+ ku Padani-aramu, nʼkunyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani kwa Isaki bambo ake.+
3 Farao anafunsa abale ake a Yosefe aja kuti: “Kodi mumagwira ntchito yanji?” Iwo anayankha Farao kuti: “Akapolo anufe timaweta nkhosa ngati mmene ankachitira makolo athu.”+