Salimo 78:40, 41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Nthawi zambiri iwo ankamupandukira mʼchipululu,+Ndipo ankamukhumudwitsa mʼchipululumo!+ 41 Ankayesa Mulungu mobwerezabwereza,+Ndipo ankachititsa kuti Woyera wa Isiraeli amve chisoni.*
40 Nthawi zambiri iwo ankamupandukira mʼchipululu,+Ndipo ankamukhumudwitsa mʼchipululumo!+ 41 Ankayesa Mulungu mobwerezabwereza,+Ndipo ankachititsa kuti Woyera wa Isiraeli amve chisoni.*