Genesis 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nyama zosadetsedwa zamtundu uliwonse utengepo zokwanira 7,*+ yaimuna ndi yaikazi yake. Koma pa nyama zodetsedwa zilizonse utengepo ziwiri zokha, yaimuna ndi yaikazi yake.
2 Pa nyama zosadetsedwa zamtundu uliwonse utengepo zokwanira 7,*+ yaimuna ndi yaikazi yake. Koma pa nyama zodetsedwa zilizonse utengepo ziwiri zokha, yaimuna ndi yaikazi yake.