Genesis 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Nowa anamangira Yehova guwa lansembe.+ Atatero, anatenga zina mwa nyama zonse zosadetsedwa, ndi zina mwa zouluka zonse zosadetsedwa,+ nʼkuzipereka nsembe yopsereza paguwapo.+
20 Kenako Nowa anamangira Yehova guwa lansembe.+ Atatero, anatenga zina mwa nyama zonse zosadetsedwa, ndi zina mwa zouluka zonse zosadetsedwa,+ nʼkuzipereka nsembe yopsereza paguwapo.+