Genesis 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Mulungu anaseseratu chamoyo chilichonse chimene chinali padziko lapansi, kuyambira munthu, nyama, nyama zokwawa komanso zamoyo zouluka mumlengalenga. Zonsezi anazisesa padziko lapansi.+ Nowa yekha komanso amene anali naye limodzi mʼchingalawacho, anapulumuka.+ Genesis 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso, zamoyo zilizonse, nyama zilizonse zokwawa, zamoyo zouluka zilizonse, chilichonse chimene chimayenda padziko lapansi, zinatuluka mʼchingalawamo monga mwa magulu awo.+
23 Choncho Mulungu anaseseratu chamoyo chilichonse chimene chinali padziko lapansi, kuyambira munthu, nyama, nyama zokwawa komanso zamoyo zouluka mumlengalenga. Zonsezi anazisesa padziko lapansi.+ Nowa yekha komanso amene anali naye limodzi mʼchingalawacho, anapulumuka.+
19 Komanso, zamoyo zilizonse, nyama zilizonse zokwawa, zamoyo zouluka zilizonse, chilichonse chimene chimayenda padziko lapansi, zinatuluka mʼchingalawamo monga mwa magulu awo.+