-
Genesis 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho Yehova anati: “Ndidzaseseratu padziko lapansi anthu amene ndinawalenga. Ndidzaseseratu anthu, nyama zoweta, nyama zokwawa komanso zamoyo zouluka mumlengalenga, chifukwa ndikumva chisoni kuti ndinazipanga.”
-