Genesis 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndikuchita pangano ndi iwe. Iweyo udzalowe mʼchingalawacho limodzi ndi ana ako, mkazi wako ndi akazi a ana ako.+ 1 Petulo 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mizimuyi sinamvere Mulungu pa nthawi imene ankaleza mtima mʼmasiku a Nowa.+ Pa nthawiyo, Nowa ankapanga chingalawa+ chomwe chinapulumutsa pamadzi anthu owerengeka, anthu* 8 okha basi.+ 2 Petulo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu sanalekerere dziko lakale lija osalipatsa chilango,+ koma anasunga Nowa, yemwe ankalalikira za chilungamo cha Mulungu.+ Anamupulumutsa limodzi ndi anthu enanso 7,+ pamene anabweretsa chigumula padziko la anthu osaopa Mulungu.+
18 Ndikuchita pangano ndi iwe. Iweyo udzalowe mʼchingalawacho limodzi ndi ana ako, mkazi wako ndi akazi a ana ako.+
20 Mizimuyi sinamvere Mulungu pa nthawi imene ankaleza mtima mʼmasiku a Nowa.+ Pa nthawiyo, Nowa ankapanga chingalawa+ chomwe chinapulumutsa pamadzi anthu owerengeka, anthu* 8 okha basi.+
5 Mulungu sanalekerere dziko lakale lija osalipatsa chilango,+ koma anasunga Nowa, yemwe ankalalikira za chilungamo cha Mulungu.+ Anamupulumutsa limodzi ndi anthu enanso 7,+ pamene anabweretsa chigumula padziko la anthu osaopa Mulungu.+