Genesis 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa tsiku limenelo Nowa analowa mʼchingalawacho. Analowa limodzi ndi ana ake Semu, Hamu ndi Yafeti,+ ndiponso mkazi wake ndi akazi atatu a ana akewo.+
13 Pa tsiku limenelo Nowa analowa mʼchingalawacho. Analowa limodzi ndi ana ake Semu, Hamu ndi Yafeti,+ ndiponso mkazi wake ndi akazi atatu a ana akewo.+