Genesis 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Mulungu ananena kuti: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi kuti madziwo+ alekane.” Genesis 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Mulungu anati: “Madzi apadziko lapansi akhale pamalo amodzi kuti mtunda uonekere.”+ Ndipo zinaterodi.
9 Kenako Mulungu anati: “Madzi apadziko lapansi akhale pamalo amodzi kuti mtunda uonekere.”+ Ndipo zinaterodi.