Genesis 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nyama zosadetsedwa zamtundu uliwonse utengepo zokwanira 7,*+ yaimuna ndi yaikazi yake. Koma pa nyama zodetsedwa zilizonse utengepo ziwiri zokha, yaimuna ndi yaikazi yake. Levitiko 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Muzisiyanitsa nyama yoyera ndi yodetsedwa, mbalame yodetsedwa ndi yoyera.+ Musadziipitse ndi nyama, mbalame kapena chilichonse chokwawa padziko lapansi chimene ndanena kuti ndi chodetsedwa.+
2 Pa nyama zosadetsedwa zamtundu uliwonse utengepo zokwanira 7,*+ yaimuna ndi yaikazi yake. Koma pa nyama zodetsedwa zilizonse utengepo ziwiri zokha, yaimuna ndi yaikazi yake.
25 Muzisiyanitsa nyama yoyera ndi yodetsedwa, mbalame yodetsedwa ndi yoyera.+ Musadziipitse ndi nyama, mbalame kapena chilichonse chokwawa padziko lapansi chimene ndanena kuti ndi chodetsedwa.+