Genesis 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Mulungu anati: “Kumwamba kukhale zounikira+ kuti zilekanitse masana ndi usiku+ ndipo zidzakhala zizindikiro zosonyeza nyengo, masiku ndi zaka.+ Salimo 74:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munaika malire onse a dziko lapansi.+Munapanga nyengo yachilimwe ndi nyengo yachisanu.+ Mlaliki 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mʼbadwo umapita ndipo mʼbadwo wina umabwera,Koma dziko lapansi lidzakhalapobe mpaka kalekale.+
14 Kenako Mulungu anati: “Kumwamba kukhale zounikira+ kuti zilekanitse masana ndi usiku+ ndipo zidzakhala zizindikiro zosonyeza nyengo, masiku ndi zaka.+