Genesis 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuyambira pano mpaka mʼtsogolo, kudzala mbewu ndi kukolola sikudzatha padziko lapansi. Ndiponso nyengo yozizira ndi yotentha, chilimwe ndi chisanu, masana ndi usiku, zidzakhalapobe.”+
22 Kuyambira pano mpaka mʼtsogolo, kudzala mbewu ndi kukolola sikudzatha padziko lapansi. Ndiponso nyengo yozizira ndi yotentha, chilimwe ndi chisanu, masana ndi usiku, zidzakhalapobe.”+