3 Ndipo anamuuza kuti, ‘Samuka mʼdziko lako ndipo uchoke pakati pa abale ako. Upite kudziko limene ndidzakuonetse.’+ 4 Choncho anasamuka mʼdziko la Akasidi nʼkukakhala ku Harana. Kumeneko, bambo ake atamwalira,+ Mulungu anamuuza kuti asamukire mʼdziko lino limene inu mukukhala panopa.+