Nehemiya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu nokha ndinu Yehova.+ Munapanga kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba ndi magulu ake onse. Munapanganso dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo komanso nyanja ndi zonse zomwe zili mmenemo. Mumasunga zinthu zamoyo ndipo magulu akumwamba amakugwadirani. Salimo 146:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amene anapanga kumwamba komanso dziko lapansi,Nyanja ndiponso zonse zimene zili mmenemo,+Amene amakhala wokhulupirika nthawi zonse,+
6 Inu nokha ndinu Yehova.+ Munapanga kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba ndi magulu ake onse. Munapanganso dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo komanso nyanja ndi zonse zomwe zili mmenemo. Mumasunga zinthu zamoyo ndipo magulu akumwamba amakugwadirani.
6 Amene anapanga kumwamba komanso dziko lapansi,Nyanja ndiponso zonse zimene zili mmenemo,+Amene amakhala wokhulupirika nthawi zonse,+